Home » Lyrics » SHARD HAAKIM – CHOKA SATANA LYRICS

SHARD HAAKIM – CHOKA SATANA LYRICS

by Malawi Gospel Music
341 views

VERSE ***1

Iwe satana.. pamalo pano
Choka choka iwe 2 Choka iwe Satana choka2
Thawi yatha iwe
Ndikufuna kupephela
Choka choka iwe
Choka iwe Satana choka***2
Pamalo pano podalisidwa
Choka choka iwe
Choka iwe Satana choka ***2

Chorus ***1

Koma undileke
Ndikufuna kulalika zayesu
Kulalika zayesu
Ndati undisiye chonde
Ndikufuna kuimbila zayesu
Kodi mvuto lako chiyani nanga
Ndikufuna kufalisa uthenga
Ndifalise uthenga
Wayesu khristu yekha
Ndikufuna kupembeza yehova
Kodi ulibe manyazi nanga?

Verse ***2

Usandiuze zaboza lako
Lakupha aii
Usandiuze zaboza lako
Lachigolo
Usandiuze za boza lako
Lakuba aiii
Usandiuze zaboza lako
Lachigololo

Chorus ***2

Athu ambiri akuzuzika
Chifukwa cha iwe
Unawapasa awa matenda
Osachidzika
Anawaphera ambale awo
Awa achikondi
Unanenela awa maboza
Lero amangidwa

Chorus ***3

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media