Home » Lyrics » RONALD THAMAKELA – DIKIRANIBE LYRICS

RONALD THAMAKELA – DIKIRANIBE LYRICS

by Malawi Gospel Music
308 views

Verse 1
Awona chilichonse nchosinthika
Mawonekedwe ulemelero wandidzadza
Wandivekanso nkhope yatsopano
Aaah aaah

Zomwe amayembekezera sizinatheke
Wawachititsa manyazi Mulungu wanga
Dzenje lomwe anakumba agweramo okha
Aaah aaah

Nsanje, kaduka, phula mmaso mwawo
Zidamata kalekale
Sangawone ubwino wanga
Kwawo ndikunyoza basi

Chorus
Pomwe mudikira kuona kugwa kwanga
Ndipomwe Mbuye akungodidalitsabe
Pomwe mudikira kuona kugwa kwanga
Ndipmwe Mbuye akungondidalitsabe
Badikiranibe
Badikiranibe
Bandikiranibe mbuye sangasiye `ndidalitsa poti mumandida inu

Verse 2
Adani anga nthawi zonse londolondo
Dobvu chuchu ngati nkango wanja
Kuti ndikangogwa andilikhwire
Aaah aaah

Koma mbuye wanga ayi sangalore
Ine ndili chete adzamenya nkhondo
Dzanja lake lamphamvu liri pa ine
Aaah aaah

Akatchera makhwekhwe, akodwamo okha
Akakumba mayenje, agweramo okha
Akapanga choipa, chimawatsata okha
Samadziwa kuti ndili ndi Yesu ineee


Chorus


Pomwe mudikira kuona kugwa kwanga
Ndipomwe Mbuye akungodidalitsabe
Pomwe mudikira kuona kugwa kwanga
Ndipomwe Mbuye akungondidalitsabe
Badikiranibe
Badikiranibe
Bandikiranibe mbuye sangasiye ndidalitsa poti mumandida inu Chorus Pomwe mudikira kuona kugwa kwanga Ndipomwe Mbuye akungodidalitsabe Pomwe mudikira kuona kugwa kwanga Ndipmwe Mbuye akungondidalitsabe Badikiranibe Badikiranibe Bandikiranibe mbuye sangasiyendidalitsa poti mumandida inu

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media