Home » Lyrics » Praise Pemphero Kambela – Sindikwanitsa Lyrics

Praise Pemphero Kambela – Sindikwanitsa Lyrics

by Malawi Gospel Music
504 views

Verse (1)

Ndikayang’ana ine,
Dziko layipaili,
Ndikayang’ana,
Dziko lasokonekera ili,
Ndikayang’ana ine,
Dzikolavuta,
Kulephera kusiyanitsa
Wachikunja
Ndiwopemphera.x2

 *chorus*

Moyowu,
pandekha sindikwanitsa
Moyowu,
Pandekha
Ndalephera ine,
Gwireni dzanja
Pandekha Sindikwanitsa,
Gwireni dzanja
Ndiwoloke sidyalo.

Verse (2)

Mukanapanda
Kukhala nane
Yehova,
Mukanapanda
Kukhala nane
Messiah!
Pakundiukira ine,
adanianga,
Akanandimeza
Ndithudi wamoyo.x2

Chorus

Moyowu
Pandekha sindikwanitsa,
Moyowu
Pandekha ndalephera ine,
Gwireni dzanja,
Pandekha sindikwanitsa,
Gwireni dzanja
Ndiwoloke sidyalo.x2

verse (3)

Chikhristu
Chopandainu
M’chachabe,
Kukhala moyo
Opanda inu
M’kowophsya!!
Ambuye musalole
Kuti ndigwe
M’manjamwanu,
Gwireni dzanja
Ndikafike sidyalo.x2

Chorous

Moyowu
Pandekha sindikwanitsa,
Moyowu
Pandekha
Ndalephera ine,
Gwireni dzanja
Pandekha Sindikwanitsa,
Gwireni dzanja
Tiwoloke sidyalo.

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media