Home » Lyrics » Praise Pemphero Kambela – Oyera Lyrics

Praise Pemphero Kambela – Oyera Lyrics

by Malawi Gospel Music
492 views

Verse 1

Ndaona ukulu wanu
Mwandionjola
Kumisampha
yomwe adani
Anatchela pa Moyo wangaaa
Dzenje lomwe anakumba
Kuti ndigwere
Inu Yaweh simunalole
Mapeto ake eeeh
Agweramo okhaa
Palibe chida
Chosuliridwa Moyo wanga
Chidzapindule popeza inu
Mesiya mulinane

Chorus

Oyera
Oyera
Oyera
Ndinu Ambuye Yehova
Wamakamu

Verse 2

Ndinu wamkulu Ambuye
Mwayeneladi ulemu onse
Ndi matamando
Ku nthawi za nthawi zonse
Bondo lonse ligwadire inu
Lilime nalo livomereze
Kuti Ambuye ndinu Mfumu
Ya Mafumu
Ine ndagoma nanu
Zintchito zanu zandidabwitsa
Njira zanuuu sinjira zathu

Chorus

Oyera
Oyera
Oyera
Ndinu Ambuye Yehova Wamakamu

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media