*chorus*
Munyengozonsee,
Zonsee, inu ndinu Mulungu,x2
Simumasintha,
Munaliko muliyemweyo,
Kunthawizonse,
Simumasintha,
Mudzakhala m’paka mpakamuyaya.
Verse-(1)
Ndikudziwa, kulimapiri otindikweleee,!!
Ndikudziwa, kulimitsinje yoti ndiwolokee!!
Chomwe ndidziwa,
Simudzalola
phadzilanga litelelekeee!!
Chomwe ndidziwa,
Simudzalola,
Adanianga atsekeleee!!
Chomwe chilichanga,
Chidzakhalabe changaa!!
Palibe nyengo,
Yomwe idzabwele,
Yopotsa mtsikhuwangaa,!!
Nthawi imasintha,
Nyengo imasinthaaa!!
Dziko limasintha,
Koma Yehova ndinu wachikhalile.
Chorus
Munyengozonsee,
zonsee,
Inu ndinu Mulungu,x2
Simumasintha,
Munaliko muliyemweyo,
Kunthawizonse,
Simumasintha,
Mudzakhala m’paka
Muyaya.
*Verse-(2)*
Abwenzi apadziko,
amakukonda Pamene
dzikuyendaa,
Koma zikathina!
onsewo amabalalikaa,!!
Nthawi imasintha,
Nyengo imasinthaa,
Dziko limasintha,
Koma Yehova,
Ndinu wachikhalile.x2
Chorus
Munyengozonsee,
Zonsee,
Inu ndinu Mulungu,x2
Simumasintha,
Munaliko muliyemweyo,
Kunthawizonse,
Simasintha mudzakhala,
M’paka Muyaya.