Ineyo mbuye yesu alinane mapulani
Ndine Testimony..Ndine Testimony
Ndikaona Dzana langa and compare today
Ndine Testimony..Ndine testimony
Testimony Testimony Ndine Testimony
Na na na
Testimony Testimony ndine TESTIMONY
Zoti dzikoli anthu amakondedwa
Chikondi ndachiziwila painu Yahweh
Zoti anthu amakhala ndi makobili
Makobili ndawaziwa ndiinu Yahweh
Mwanditola / Mwandisambitsa / Mwandiyeretsa
Manditchenetsa / Mwandikweza / Mwandilemekeza
Kale langa linali la chisoni
Koma lero mwandipanga umboni
I just wanna say thank you Lord
Chifundo ndachionela pa inu yahweh
Chisomo ndachiziwila paninu Yahweh
Ndinali Kape opanda pake popanda inu yesu
Youre my number 1 ..Youre one ina million
You have made me a Testimony
Ndine umboni my my my my
Testimony Testimony ndine TESTIMONY
Na na na Testimony Testimony Ndine Testimony
Ineyo mbuye yesu alinane mapulani
Ndine Testimony..Ndine Testimony
Ndikaona Dzana langa and compare today
Ndine Testimony..Ndine testimony
Testimony Testimony Ndine Testimony
Testimony Testimony ndine TESTIMONY