Home » Lyrics » GODFREY PSALMIST ZULU – UDZATSALA WEKHA LYRICS

GODFREY PSALMIST ZULU – UDZATSALA WEKHA LYRICS

by Malawi Gospel Music
779 views

Chorus

Zochita zako ndi zako
Ngati sumva zako
Udzatsala wekha kumwamba
Chipulumutso ndiwekha

Story 1


Sizotengera chigulu
Sizotsatira anzako izi
Sizopikisananso ayi
Opita kosiyana
Paja sapikisana
Wachita bwanji kodi
Unakali pasukulu
Mwai ophunzira uli nawo
Okuthandiza anakalipo
Nzeru unakali nazo
Koma wasankha kuipsa moyo
Mu m’dzina losafuna kufinyika
Ndiye wapangatu zonse

Story 2

Umkatchedwa okongola
Unali kangenge
Kopangitsa dzanzi obongo wa amuna
Umadzitchula slay queen
Life inali better mkuona kwako
Lero zakutsalira
Za mawa sumkaganizako
Umkaseweretsa moyo
Umvekere ukunjoya
Unatchuka inde
Anthu onse amkanena za iwe
Unali dolo pakati pa anzako
Tsano wasanduka kape
Wakhale choseweretsa

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media