Chorus
Pemphelo losweka mtimalimasintha zinthu, pemphelo losweka mtima limachilitsa, pemphelo losweka mtima limasintha nyengo, pemphelo likhale chida chako
Verse 1
Nkhondo ya uzimu siyofunika zibonga, mfuti ndi mikondo ayi, koma nkhondo ya uzimu ndiyofunika Baibolu ndiso pemphelo *2
Chorus
Pemphelo losweka mtimalimasintha zinthu, pemphelo losweka mtima limachilitsa, pemphelo losweka mtimalimasintha nyengu, pemphelo likhale chida chako.
Verse 2
Mubale limbikira ndikupemphela or akunyodze akutukwane iwe, koma tsiku lina udzayimba nyimbo yachitsangalo *2