Home » Lyrics » Atlas Kaliwungo (Mr Me) – Pemphelo Losweka Mtima Lyrics

Atlas Kaliwungo (Mr Me) – Pemphelo Losweka Mtima Lyrics

by Malawi Gospel Music
397 views

Chorus

Pemphelo losweka mtimalimasintha zinthu, pemphelo losweka mtima limachilitsa, pemphelo losweka mtima limasintha nyengo, pemphelo likhale chida chako

Verse 1

Nkhondo ya uzimu siyofunika zibonga, mfuti ndi mikondo ayi, koma nkhondo ya uzimu ndiyofunika Baibolu ndiso pemphelo *2

Chorus

Pemphelo losweka mtimalimasintha zinthu, pemphelo losweka mtima limachilitsa, pemphelo losweka mtimalimasintha nyengu, pemphelo likhale chida chako.

Verse 2

Mubale limbikira ndikupemphela or akunyodze akutukwane iwe, koma tsiku lina udzayimba nyimbo yachitsangalo *2

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media