Vol 2.
Verse 1.
Dziko lino lapasi muli zinthu zambili,muli kusangalala komanso ndikulila komano kwayesuyo kulimoyo wosatha, ukalapa machimo udzalandila yesu,nthawi musewelesai ena mmatembelelo,nthawi musewelesai kwaena akudalitsika,nthawi musewelesai ena akumwalila nthawi yokhayokhayo ena akulapa tchimooo
Chorus
Iwe lapa m baleee
nthawi yako isanathe
Siya tchimo
nthawi Yako ndiyomwei
Iwe lapa m bale
nthawi Yako isanathe
Lapalapa
nthawi Yako ndiyomwei
Iwe lapa m bale!!
nthawi yako isanathe
Siya tchimo
nthawi Yako ndiyomwei
Iwe lapa m bale
nthawi Yako isanathe
Siya bodza
nthawi Yako ndiyomwei
Iwe lapa m bale,Siya kuba
nthawi Yako isanathe
Iwe lapa m bale lapalapa
nthawi Yako ndiyomwei
Verse 2.
Nthawi ino abale siyochedwa ndi tchimo,nthawi ino abale ndiyolandila yesu ,nthawi ino anabe siyongodandaula,nthawi yokhayokhayo ena alandile yesu,tikamakhala abale tidziwe kuli mulungu konse kumene tiyenda ngakhale pa babja pathu,tikamachita machimo tiziwe mbuye amaona,Mulungu ndiye mzimu amaona ponsepoooo
Verse 3.
Dziko lino lapasi muli zinthu zambili muli kusangalala komaso ndikulila komano kwayesuyo kuli moyo wosatha,ukalapa machimo udzalandila yesu,nthawi musewelesai ena mmatembelelo,nthawi musewelesai kwa ena akudalisika,nthawi musewelesai ena akumwalila,nthawi yokhayokhayo ena akulapa tchimoo