Verse***1
Ndikulira ine***x4
Mtima wanga ukupweteka
Ndichian chikuchitika
Kubanja langa linali khomo
Lonyadisa losangalasa
Ndikanjoya ndi katumbwa
Poziwa kuti ndili khomo
Lelolino abale anga
Achikondi apatima
Andisiya ndasala ndekha
Ndikondwa bwanji
Popanda bale
Chorus ***1
Ine ndikulira
Ndikulira ine mbuye wanga
Koma kalanga ine
Ndikulira ine mbuye wanga
Inu amama
Ndikulira ine mbuye wanga
Ine ndikulira ineyoo
Ndikulira ine mbale wanga
Verse ***2
Ndikachoka kutauni
Wakumudzi kaone athu
Ndikangofika athu onse
Kusangalala kuluphalupha
Mbale uu inu wabwela
Akandiphela ichi chikhuku
Zinali zithu zonyadisa
Pachiyambi ndi moyo wanga***2
Chorus …2
Ine ndikulira
Komandikulira ineoo e ..ee..ee
Eti kalanga ineoo…aaaa
Ndasala ndekha ineoo ….hh
Verse ***3
Mai wanga anapita
Achimwene anapita
Chemwali wanga anapita
Nzukulu wanga anapita
Ndikawafusa achibale
Sakundiyakha zogwira mutu
Iwe mbale usalire
Uyu ndye kwake kwapita
Moto uwu umapita
Kwasala tchile iwe mwananga
Mulungu ndiye wamukonda
Ziyang’anile mwa iwe wekha
Chorus number ***2
Verse**2
Banja langa lasala bwinja
Kukundivuta ķukafikako
Mtima wanga ukupweteka
Misozi ndiye yoasalekeza
Mbuye wanga ndikupepha
Mundipase banja lina
Ndikamakhala ndizinyada
Ndizikondwa monga poyamba***x2
Chorus number one