VERSE ***1
Pasiku lomaliza
M’bale wanga2 Lipenga likangolira Wakumoto2
Angelo akangotsika
Kuchoka kumwambako
Lipenga Lao manja
Iwe likangolira
Palibe kugwada pansi
Iwe kulapa ntchimo
Iwe bale wanga
Wakumoto
Chorus ***1
Ine ndasikimiza
Iwe wakumoto
Ngatitu sukulapa
Eeee..aye Wakumoto
Iwe mbale wanga
Iwe Wakumoto
Ndatitu Wakumoto
Eeee..ayee wakumoto
Ine ndasikimiza
Iwee wakumoto
Ngatitu sukulapa
Eeee..ayee wakumoto
Iwe wakumoto
Iwe wakumoto
Ine ndasikimiza
Eee..aye wakumoto
VERSE ***2
Iwe mbale wanga ndati ndikuuze
Nthawi ndye yomwei
Iwe ulapiletu
Kaya ndi wakuba
Kaya ndiwakupha
Wachigololo
Ozuza azake
Angelo akangosika
Kuchoka kumwambako
Iwo azauluka
Umo mulengalenga
Lipenga likangolira
Palibe kugwada pansi
Ine ndasikimiza
Chorus ***3