Chifundo Matengo Fundi anabadwa pa 15 January 1989 ndipo m’banja la kwawo kunabadwa ana atatu ndipo iye ndi oyamba kubadwa.

Chifundo anayamba kuyimba mu chaka cha 2019 ndipo anakhazikitsa chimbale chake chotchedwa Adzatimenyera Nkhondo mu 2021 ndipo pakadali pano akujambula chimbale chake chachiwiri.